Ndizakukwatira
Giboh Pearson
4:29It's Driemo Mmmh I say beauty yofunika medal Timaso tokoka attention Akamayenda ngati sanachimwepo Polenga iwe ankaona angelo M'maso mwanga ndamunveka vero Koma olo dzina langa sanalimvepo Zoti amandidziwa sindinganenepo Awa ndi makina machine amphepo Uyu ndi ndi mankhwala ozunguza bongo Ona mpaka shasha wapinda mabondo Kaya ikhala nkhondo tisenza mikondo Kaya sandimvera tikaona konko ooh Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa This girl is out of my league She's out of my league This girl is out of my league She's out of my league yah Ali champions ndili mu super league Ndili mu disco iye super gigi Mu bus yake sindingapezemo seat Ndili panja sitingachite link Call me a soldier ndili pa mission Never give up ndili ndi reason Zikangovuta nditenga commission Koma for now mayiwa ndi mission Uyu ndi ndi mankhwala ozunguza bongo Ona mpaka shasha wapinda mabondo Kaya ikhala nkhondo tisenza mikondo Kaya sandimvera tikaona konko ooh Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa This girl is out of my league She's out of my league This girl is out of my league She's out of my league yah To be honest zosiyana nzambiri Zolekana nzambiri Bwanji ndizisiye ndingaononge mbiri Ndazipatsa malire To be honest zosiyana nzambiri Zolekana nzambiri Bwanji ndizisiye ndingaononge mbiri Ndazipatsa malire Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa This girl is out of my league She's out of my league This girl is out of my league She's out of my league yah Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa This girl is out of my league She's out of my league This girl is out of my league She's out of my league yah