Lere (Feat. Skeffa Chimoto)
Driemo Mw
4:11Ndipatsireni pen paper ndimulembere mwali Mwina ndikatenge mic ndiyimbe Mwina tiyesere ma blocko poti njerwa zimagumuka Koma bola tichimange chilimbe Wazipereka nsembe kwakwana mamuna sayamika uyu nde atipatsire ife tisunge Ngati watopa nawe Asiye kukuzunguza, bola ativungire cross tigwire Poti chikondi sikundende You supposed to be loved babe Chikondi kumapeto Poti chikondi sikundende You supposed to be loved babe Chikondi kuma last Nde udzabwere eh Bwere eeee zanga (If you're not happy anymore) Nde udzabwere eh Bwere eeee zanga (If you're not happy anymore) Come to me babe Poti Matambala ndi nono Olo kukhala kungokhalira zisomo mama Mumtima muli nkhondo Pali kutsutsana pakati pamikoko eee Sangasinthe Sangasiye olo utati bwanji Wa chake ndi wachake Mamie bola mungosintha plan Amakuzembera zembera Khutu unatseka nde zimavuta kunvera Ukamufunsa amakumemya Unagwidwa ndi ndende nde ufulu umakuthera Nobody cares Nobody cares ungasinthe eee Nobody cares Nobody cares ungasinthe eee Ati chikondi Ndikupilira Upilira bwanji zopilirazo palibe Let me take your pain away Let me your dream guy Poti chikondi sikundende You supposed to be loved babe Chikondi kumapeto Poti chikondi sikundende You supposed to be loved babe Chikondi kuma last Nde udzabwere eh Bwere eeee zanga (If you're not happy anymore) Nde udzabwere eh Bwere eeee zanga (If you're not happy anymore) Come to me babe