Magini
Driemo Mw
3:12Pento maker yamoyo wanga Rain ball colour muchalo changa Water in my desert flower Unkhale queen in my kingdom Make your voice be my ringtone Nyimbo ndalembera iwe Akafunsa love ndimaloza iwe Afunse mtendere ndimaona iwe Oooh This loving ain't no more Wayambitsa nkhondo How beautiful you are my dear That's why I say Ngati okonda anatha (Utangodikira nde uwone) Ngati chikondi chinatha (Utangopilira ndikuonetse) Eh This is a reborn (Ole my babe) This is a reborn (Ole eh) This is a reason Yokondera mwali iwee they thought that love was dead till I met you I thought that love was fake till I met you Uli na mutima wokonda Uli na mutima onvera (that's why I say Ngati okonda anatha (Utangodikira nde uwone) Ngati chikondi chinatha (Utangopilira ndikuonetse) Eh This is a reborn (Ole my babe) This is a reborn (Ole eh) This is a reason Yokondera mwali iwee