Out Of My League
Driemo Mw
3:28Uh yeah yeah Mama pick up the phone I really need someone to talk to Mama pick the phone yeah Cause your son is in battles I don't really know if I can win this All I need is your wisdom uh yeah Dziko ladzadza ndima bonzo Kukhalira chitonzo I don't really know kani zimakhala choncho Ndifuna mundigwire nkono Oooh! Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine eee Mama answer my questions Cause I don't know the reasons Why people are faking love Faking happy life Kubisala muzithunzi zosekerera Kuseli akunjenjemera Nobody Nobody seems real Aliyense ali choncho (Nde) Zikadzandivuta mayiwanga Mudzandiitane mwana wanga bwera bwera Bwera There is light At the end of this tunnel Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine eee Mayi mukapinda bondo Mukapinda bondo Mamie mukapinda bondo Mukapinda bondo Mapemphero amayankhidwa Zitseko zimatsekuka Mayi mukapinda bondo So pray for me! Mama Pray for me! Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine eee Mama pray for me Pray for me konse ndingayende ine Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for memudzindipempherera! Mama pray for me Pray for me